Isaiah 3:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho pa zipata zako padzakhala kulira kokhakokha, iweyo udzasakazidwa nkukhala pansi, ukuvimvinizika pa fumbi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zipata zake zidzalira maliro; ndipo iye adzakhala bwinja, nadzakhala pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa zipata za Ziyoni padzakhala kubuma ndi kulira; Iweyo udzasakazidwa nʼkukhala pansi, ukugubuduzika pa fumbi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zipata zace zidzalira maiko; ndipo iye adzakhala bwinja, nadzakhala pansi.