Isaiah 3:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzaŵaikira anyamata kuti akhale mafumu ao, ndipo ana amakanda ndiwo adzaŵalamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzapereka ana, kuti akhale akulu ao, mwachibwana adzawalamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawayikira anyamata kuti akhale mafumu awo; ana akhanda ndiwo adzawalamulire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzapereka ana, kuti akhale akuru ao, mwacibwana adzawalamulira.