Isaiah 3:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu adzagwira mbale wake m'nyumba ya atate ao, nkunena kuti, “Iwe uli nawo mwinjiro, ndiye ukhale mtsogoleri wathu nthaŵi yamavutoyi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene mwamuna adzamgwira mbale wake m'nyumba ya atate wake, nadzati, Iwe uli ndi chovala, khala wolamulira wathu, ndi kupasula kumeneku kukhale m'dzanja lako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu adzagwira mʼbale wake mʼnyumba ya abambo awo, ndipo adzati, “Iwe uli nawo mwinjiro, ndiye ukhale mtsogoleri wathu; lamulira malo opasuka ano!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene mwamuna adzamgwira mbale wace m'nyumba ya atate wace, nadzati, Iwe uli ndi cobvala, khala wolamulira wathu, ndi kupasula kumeneku kukhale m'dzanja lako;