Isaiah 30:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kutchinjiriza kwa Farao kudzakuchititsani manyazi, ndipo malo opulumukirako a ku Ejipitowo mudzachita nawo manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake mphamvu za Farao zidzakhala kwa inu manyazi, ndi kukhulupirira mthunzi wa Ejipito kudzakhala chisokonezo chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma chitetezo cha Farao chidzakhala manyazi anu, malo a mthunzi a ku Igupto mudzachita nawo manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace mphamvu za Farao zidzakhala kwa inu manyazi, ndi kukhulupirira mthunzi wa Aigupto kudzakhala cisokonezo canu.