Isaiah 30:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
anthu onse a ku Yuda adzamva manyazi chifukwa cha anthu opanda nawo phindu ndipo osaŵathandiza konse, koma ongobweretsa manyazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo onse adzakhala ndi manyazi, ndi anthu amene sangapindule nao kanthu, amene sakhala kwa iwo thangata, pena phindu, koma manyazi ndi chitonzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
aliyense wa ku Yuda adzachita manyazi chifukwa cha anthu opanda nawo phindu, amene sabweretsa thandizo kapena phindu, koma manyazi ndi mnyozo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo onse adzakhala ndi manyazi, ndi anthu amene sangapindule nao kanthu, amene sakhala kwa iwo thangata, pena phindu, koma manyazi ndi citonzo.