Isaiah 30:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa ndi anthu opandukira Mulungu, ana onama, okana kumvera malangizo a Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ali anthu opanduka, ana onama, ana osafuna kumva chilamulo cha Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amenewa ndi anthu owukira, onama ndi osafuna kumvera malangizo a Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ali anthu opanduka, ana onama, ana osafuna kumva cilamulo ca Yehova;