Isaiah 32:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi ina kudzakhala mfumu ina yolamulira mwaungwiro, ndiponso nduna zina zoweruza mwachilungamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani mfumu idzalamulira m'chilungamo, ndi akalonga adzalamulira m'chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, kudzakhala mfumu ina imene idzalamulira mwachilungamo, ndipo akalonga ake adzaweruza molungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani mfumu idzalamulira m'cilungamo, ndi akalonga adzalamulira m'ciweruzo.