Isaiah 32:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakapita chaka ndi masiku pang'ono, mudzanjenjemera inu akazi amatama, chifukwa mitengo ya mphesa idzakanika, zipatsonso sizidzaoneka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutha chaka, kudza masiku ena inu mudzavutidwa, inu akazi osasamalira; pakuti masika a mphesa adzasoweka, sadzatuta konse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakapita chaka ndi masiku pangʼono inu akazi amatama mudzanjenjemera; chifukwa mitengo ya mphesa idzakanika ndipo zipatso sizidzaoneka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakutha caka, kudza masiku ena inu mudzabvutidwa, inu akazi osasamalira; pakuti masika a mphesa adzasoweka, sadzatuta konse.