Isaiah 32:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzimenyeni pa chifuŵa mwachisoni, chifukwa minda yachonde ndi yamphesa yaonongeka,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo adzadzimenya pazifuwa chifukwa cha minda yabwino, chifukwa cha mpesa wobalitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzigugudeni pachifuwa mwachisoni chifukwa minda yachonde, ndi mphesa yawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo adzadzimenya pazifuwa cifukwa ca minda yabwino, cifukwa ca mpesa wobalitsa.