Isaiah 32:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo minga ndi mkandankhuku zikumera pa dziko la anthu anga. Ndithu, mulire nyumba zonse zimene ankakhalamo mosangalala, ndiponso mzinda umene udaali ndi chimwemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa dziko la anthu anga padzafika minga ndi lunguzi; inde pa nyumba zonse zokondwa, m'mudzi wokondwerera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼdziko la anthu anga mwamera minga ndi mkandankhuku. Zoona, mulilire nyumba zonse zachikondwerero ndi mzinda uno umene unali wachisangalalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa dziko la anthu anga padzafika minga ndi lunguzi; inde pa nyumba zonse zokondwa, m'mudzi wokondwerera;