Isaiah 32:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe nkhalango idzaonongedwa ndi matalala, ndipo mzinda udzagwetsedwa mpaka pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kudzagwa matalala m'kugwa kwake kwa nkhalango; ndipo mudzi udzagwetsedwa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale nkhalango idzawonongedwa ndi matalala ndipo mzinda udzagwetsedwa mpaka pansi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kudzagwa matalala m'kugwa kwace kwa nkhalango; ndipo mudzi udzagwetsedwa ndithu.