Isaiah 32:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adzakondwa kwambiri chifukwa adzakhala ndi madzi ambiri, ndipo abulu ndi ng'ombe zao azidzadya paliponse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odala muli inu, amene mubzala m'mbali mwa madzi monse, amene muyendetsa mapazi a ng'ombe ndi bulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
inutu mudzakhala odalitsika ndithu. Mudzadzala mbewu zanu mʼmbali mwa mtsinje uliwonse, ndipo ngʼombe zanu ndi abulu anu zidzadya paliponse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odala muli inu, amene mubzala m'mbali mwa madzi monse, amene muyendetsa mapazi a ng'ombe ndi buru.