Isaiah 32:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mtima waphamphu adzadziŵa kuchita zinthu moganiza bwino, ndipo anthu achibwibwi adzalankhula mosadodoma ndi momveka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtimanso wansontho udzadziwa nzeru, ndi lilime la achibwibwi lidzalankhula zomveka msanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a mtima wopupuluma adzadziwa ndi kuchita zinthu mofatsa, ndipo anthu ovutika kuyankhula adzayankhula mosadodoma ndi momveka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtimanso wansontho udzadziwa nzeru, ndi lilume la acibwibwi lidzalankhula zomveka msanga.