Isaiah 34:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuluakulu sadzasankhanso mfumu kumeneko, ndipo atsogoleri ake onse adzakhala atachotsedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo adzaitana mfulu zake zilowe m'ufumu, koma sizidzaonekako; ndi akalonga ake onse adzakhala chabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olemekezeka ake sadzatchedwanso mfumu kumeneko; akalonga ake onse adzachotsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo adzaitana mfulu zace zilowe m'ufumu, koma sizidzaonekako; ndi akalonga ace onse adzakhala cabe.