Isaiah 34:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imeneyi ndiyo nthaŵi imene Chauta adzalipsira, pamene adzalanga adani a Ziyoni, ndi kuteteza anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti lili tsiku la kubwezera la Yehova, chaka chakubwezera chilango, mlandu wa Ziyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyi ndi nthawi imene Yehova adzalipsira ndi kulanga adani a Ziyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti liri tsiku la kubwezera la Yehova, caka cakubwezera cilango, mlandu wa Ziyoni.