Isaiah 35:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chipululu ndi dziko lopanda madzi zidzasangalala, dziko louma lidzakondwa ndi kuchita maluŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chipululu ndi malo ouma adzakondwa; ndipo dziko loti see lidzasangalala ndi kuphuka ngati duwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chipululu ndi dziko lopanda madzi zidzasangalala; dziko lowuma lidzakondwa ndi kuchita maluwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cipululu ndi malo ouma adzakondwa; ndipo dziko loti se lidzasangalala ndi kuphuka ngati duwa.