Isaiah 35:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mchenga wotentha udzasanduka nyanja, ndipo dziko louma lidzasanduka la akasupe. Pamene panali mbuto za nkhandwe padzamera udzu ndi bango.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mchenga wong'azimira udzasanduka thamanda, ndi nthaka yopanda madzi idzasanduka zitsime zamadzi; m'malo a ankhandwe m'mene iwo anagona, mudzakhala udzu ndi mabango ndi milulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mchenga wotentha udzasanduka dziwe, nthaka yowuma idzasanduka ya akasupe. Pamene panali mbuto ya ankhandwe padzamera udzu ndi bango.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mcenga wong'azimira udzasanduka thamanda, ndi nthaka yopanda madzi idzasanduka zitsime zamadzi; m'malo a ankhandwe m'mene iwo anagona, mudzakhala udzu ndi mabango ndi milulu.