Isaiah 37:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga mafumu a m'mizinda ya Hamati, Aripadi, Sefaravaimu, Hena ndi Iva, ali kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ili kuti mfumu ya ku Hamati, ndi mfumu ya ku Aripadi, ndi mfumu yamudzi wa ku Sefaravaimu, ya ku Hena, ndi Iva?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mafumu a ku Hamati, Aripadi, Safaravaimu, Hena ndi Iva ali kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iri kuti mfumu ya ku Hamati, ndi mfumu ya ku Aripadi, ndi mfumu yamudzi wa ku Sefaravaimu, ya ku Hena, ndi Iveva?