Isaiah 37:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adatuma Eliyakimu mkulu wa nyumba ya mfumu, Sebina mlembi wa mfumu, ndiponso ansembe akuluakulu, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya, mwana wa Amozi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatumiza Eliyakimu, wapanyumba, ndi Sebina, mlembi, ndi akulu a nsembe, atafunda chiguduli, kwa Yesaya, mneneri, mwana wa Amozi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatuma Eliyakimu woyangʼanira nyumba ya mfumu, Sebina mlembi wa bwalo, ndi ansembe akuluakulu, onse atavala ziguduli, kwa mneneri Yesaya mwana wa Amozi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatumiza Eliakimu, wapanyumba, ndi Sebina, mlembi, ndi akuru a nsembe, atapfunda ciguduli, kwa Yesaya, mneneri, mwana wa Amozi.