Isaiah 37:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yesaya, mwana wa Amozi, adatumiza kwa mfumu Hezekiya mau ochokera kwa Chauta, Mulungu wa Israele, oyankha pemphero lake lija lonena za Senakeribu, mfumu ya ku Asiriya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yesaya, mwana wa Amozi, anatumiza kwa Hezekiya, ndi kuti, Atero Yehova, Mulungu wa Israele, Popeza wandipemphera za Senakeribu mfumu ya Asiriya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga wochokera kwa Yehova kwa Hezekiya poyankha pemphero lake lokhudza Senakeribu mfumu ya ku Asiriya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yesaya, mwana wa Amozi, anatumiza kwa Hezekiya, ndi kuti, Atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, Popeza wandipemphera za Sanakeribu mfumu ya Asuri,