Isaiah 37:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakumba zitsime ku maiko achilendo ndi kumwamo madzi. Ndi mapazi anga ndidapondereza ndi kuumitsa mitsinje ya ku Ejipito.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndakumba ndi kumwa madzi, ndidzaumitsa nyanja zonse za Ejipito ndi kuphazi kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakumba zitsime ku mayiko achilendo ndi kumva madzi akumeneko ndi mapazi anga ndawumitsa mitsinje yonse ya ku Igupto.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndakumba ndi kumwa madzi, ndidzaumitsa nyanja zonse za Aigupto ndi kuphazi kwanga.