Isaiah 38:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Moyo wanga walandidwa ndi kuchotsedwa, ngati hema logwetsedwa, ngati nsalu yodulidwa ku makina ake oombera. Kuyambira m'maŵa mpaka usiku mwakhala mukunditsiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pokhala panga pachotsedwa, pandisunthikira monga hema wa mbusa; Ndapindapinda moyo wanga ngati muomba; Iye adzandidula ine poomberapo; Kuyambira usana kufikira usiku mudzanditsiriza ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyumba yanga yasasuka ndipo yachotsedwa. Ngati tenti ya mʼbusa mwapindapinda moyo wanga, ngati munthu wowomba nsalu; kuyambira usana mpaka usiku mwakhala mukundisiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pokhala panga pacotsedwa, pandisunthikira monga hema wambusa; Ndapindapinda moyo wanga ngati muomba; Iye adzandidula ine poomberapo; Kuyambira usana kufikira usiku mudzanditsiriza ine.