Isaiah 38:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndinganene chiyani? Chauta walankhula nane, ndipo wachita zimenezi ndiye amene. Pa moyo wanga wonse ndidzakhala wovutika, chifukwa cha kuŵaŵa kwa mtima wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ndidzanena chiyani? Iye wanena kwa ine, ndiponso Iye mwini wachita ichi; Ine ndidzayenda chete zaka zanga zonse, chifukwa cha zowawa za moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine ndinganene chiyani? Yehova wayankhula nane, ndipo Iye ndiye wachita zimenezi. Chifukwa cha kuwawa kwa mtima wanga, ine ndidzayenda modzichepetsa masiku amoyo wanga onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ndidzanena ciani? Iye wanena kwa ine, ndiponso Iye mwini wacita ici; Ine ndidzayenda cete zaka zanga zonse, Cifukwa ca zowawa za moyo wanga.