Isaiah 38:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Hezekiya adatembenuka nayang'ana ku khoma, nayamba kupemphera kwa Chauta kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hezekiya analoza nkhope yake kukhoma, napemphera kwa Yehova, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hezekiya anatembenuka nayangʼana kukhoma, napemphera kwa Yehova kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hezekiya analoza nkhope yace kukhoma, napemphera kwa Yehova, nati,