Isaiah 38:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chauta wandipulumutsa, ndipo tidzamtamanda poimba ndi azeze m'Nyumba mwa Chauta pa moyo wathu wonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye wondipulumutsa ine; Chifukwa chake tidzaimba nyimbo zanga, ndi zoimba zazingwe Masiku onse a moyo wathu m'nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova watipulumutsa. Tiyeni tiyimbe ndi zoyimbira za zingwe masiku onse a moyo wathu mʼNyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye wondipulumutsa ine; Cifukwa cace tidzayimba nyimbo zanga, ndi zoyimba zazingwe Masiku onse a moyo wathu m'nyumba ya Yehova.