Isaiah 38:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu Hezekiya adafunsa kuti, “Kodi chizindikiro chake nchiyani chotsimikizira kuti ndidzapita ku Nyumba ya Chauta?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Hezekiya anatinso, Chizindikiro nchiyani, kuti ndidzakwera kunka kunyumba ya Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hezekiya nʼkuti atafunsa kuti, “Kodi chizindikiro chako nʼchiyani chotsimikiza kuti ndidzapita ku Nyumba ya Yehova?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Hezekiya anatinso, Cizindikilo nciani, kuti ndidzakwera kunka ku nyumba ya Yehova?