Isaiah 38:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuti, ‘Chithunzithunzi chimene dzuŵa likuchititsa pa makwerero a Ahazi, ndidzachibweza m'mbuyo makwerero khumi.’ ” Ndipo chithunzithunzicho chidabwereradi m'mbuyo makwerero khumi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
taona, ndidzabweza mthunzi wa pamakwerero, umene watsika pa makwerero a Ahazi ndi dzuwa, ubwerere makwerero khumi. Ndipo dzuwa linabwerera makwerero khumi pamakwerero, pamene udatsika mthunziwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chithunzithunzi chimene dzuwa likuchititsa pa makwerero a Ahazi ndidzachibweza mʼmbuyo makwerero khumi.’ ” Ndipo chithunzithunzi chinabwerera mʼmbuyo makwerero khumi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
taona, ndidzabweza mthunzi wa pamakwerero, umene watsika pa makwerero a Ahazi ndi dzuwa, ubwerere makwerero khumi. Ndipo dzuwa linabwerera makwerero khumi pamakwerero, pamene udatsika mthunziwo.