Isaiah 38:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndakatulo ya Hezekiya mfumu ya ku Yuda, amene adaadwala kenaka nkuchira:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Malemba a Hezekiya mfumu ya Ayuda muja anadwala, atachira nthenda yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakatulo ya Hezekiya mfumu ya ku Yuda imene analemba atadwala ndi kuchira:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Malemba a Hezekiya mfumu ya Ayuda muja anadwala, atacira nthenda yace.