Isaiah 4:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono otsalira ku Ziyoni, amene Mulungu waŵasankha kuti akhale ndi moyo ku Yerusalemu, adzatchedwa oyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzakhala, kuti iye amene asiyidwa m'Ziyoni, ndi iye amene atsala m'Yerusalemu adzatchedwa woyera; ngakhale yense amene walembedwa mwa amoyo m'Yerusalemu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene adzatsale mu Ziyoni, amene adzatsalire mu Yerusalemu, adzatchedwa oyera, onse amene mayina awo alembedwa pakati pa anthu amoyo okhala mu Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzakhala, kuti iye amene asiyidwa m'Ziyoni, ndi iye amene atsala m'Yerusalemu, adzachedwa woyera; ngakhale yense amene walembedwa mwa amoyo m'Yerusalemu;