Isaiah 40:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga simudadziŵe? Monga simudamve? Kodi poyamba ponse sadakuuzeni? Kodi simudamvetse za kakhazikitsidwe ka dziko lapansi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi inu simunadziwe? Kodi inu simunamve? Kodi sanakuuzeni inu chiyambire? Kodi inu simunadziwitse chiyambire mayambiro a dziko lapansi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi simukudziwa? Kodi simunamve? Kodi sanakuwuzeni kuyambira pachiyambi pomwe? Kodi simunamvetsetse chiyambire cha dziko lapansi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi inu simunadziwe? kodi inu simunamve? kodi sanakuuzani inu ciyambire? kodi inu simunadziwitse ciyambire mayambiro a dziko lapansi?