Isaiah 40:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe Yakobe, ukulankhuliranji? Iwe, Israele, ukuneneranji kuti Chauta sakudziŵa za mavuto ako, kapenanso kuti sakusamalapo za iwe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwanji iwe, Yakobo, umati, ndi bwanji umanena iwe, Israele, Njira yanga yabisika kwa Yehova; ndipo chiweruzo cha Mulungu wanga chandipitirira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe Yakobo, chifukwa chiyani umanena ndi kumadandaula iwe Israeli, kuti, “Yehova sakudziwa mavuto anga, Mulungu wanga sakusamala zomwe zikundichitikira ine?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwanji iwe, Yakobo, umati, ndi bwanji umanena iwe, Israyeli, Njira yanga yabisika kwa Yehova; ndipo ciweruzo ca Mulungu wanga candipitirira?