Isaiah 40:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzu umauma, maluŵa amafota, Chauta akaziwuzira mpweya wake. Ndithudi anthu sasiyana ndi udzu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
udzu unyala, duwa lifota; chifukwa mpweya wa Yehova waombapo; zoonadi anthu ndi udzu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzu umanyala ndipo maluwa amafota chifukwa cha kuwomba kwa mpweya wa Yehova.” Mawu aja anatinso, “Ndithudi anthu sasiyana ndi udzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
udzu unyala, duwa lifota; cifukwa mpweya wa Yehova waombapo; zoonadi anthu ndi udzu.