Isaiah 41:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzafunafuna amene amakangana nawe, koma osaŵapeza. Amene amamenyana nawe nkhondo adzakhala ngati salinso kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe udzawafuna osawapeza, ngakhale iwo amene akangana ndi iwe; ochita nkhondo ndi iwe, adzakhala ngati chabe, ndi monga kanthu kopanda pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzafunafuna adani ako, koma sadzapezeka. Iwo amene akuchita nawe nkhondo sadzakhalanso kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe udzawafuna osawapeza, ngakhale iwo amene akangana ndi iwe; ocita nkhondo ndi iwe, adzakhala ngati cabe, ndi monga kanthu kopanda pace.