Isaiah 41:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'chipululu ndidzameretsa mkungudza, kasiya, mchisu ndi mtengo wa olivi. M'dziko louma ndidzabzala mitengo ya paini ya mitundu itatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzabzala m'chipululu mkungudza, ndi msangu, ndi kasiya, ndi mtengo wa azitona; ndidzaika m'chipululu pamodzi mlombwa, ndi mkuyu, ndi naphini;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchipululu ndidzameretsa mkungudza, kasiya mchisu ndi mtengo wa Olivi. Mʼdziko lowuma ndidzaza mitengo ya payini, ya mkuyu ndi ya mlombwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzabzala m'cipululu mkungudza, ndi msangu, ndi mcisu, ndi mtengo waazitona; ndidzaika m'cipululu pamodzi mlombwa, ndi mkuyu, ndi naphini;