Isaiah 41:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuuza milungu kuti, “Dzafotokozeni mlandu wanu.” Chauta, Mfumu ya Yakobe akuti, “Perekani umboni wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onetsani mlandu wanu, ati Yehova; tulutsani zifukwa zanu zolimba, ati mfumu ya Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova akuwuza milungu ina kuti, ‘Fotokozani mlandu wanu.’ Mfumu ya Yakobo ikuti, ‘Perekani umboni wanu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onetsani mlandu wanu, ati Yehova; turutsani zifukwa zanu zolimba, ati Mfumu ya Yakobo.