Isaiah 41:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mubwere kuno, mudzatiwuze zam'tsogolo. Mufotokozere bwalo zamakedzana, kuti tiziganizire, ndipo tidziŵe zotsatira zake, kapena mutiwuze zakutsogolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Azitulutse, atitchulire ife, chimene chidzaoneka; tchulani inu zinthu zakale, zinali zotani, kuti ife tiganizire pamenepo, ndi kudziwa mamaliziro ao; kapena tionetseni ife zinthu zimene zilinkudza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwerani ndi milungu yanu kuti idzatiwuze zomwe zidzachitike mʼtsogolo. Tifotokozereni zinthu zamakedzana tiziganizire ndi kudziwa zotsatira zake. Kapena tiwuzeni zimene zidzachitike mʼtsogolo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aziturutse, atichulire ife, cimene cidzaoneka; chulani inu zinthu zakale, zinali zotani, kuti ife tiganizire pamenepo, ndi kudziwa mamariziro ao; kapena tionetseni ife zinthu zimene zirinkudza.