Isaiah 41:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inuyo sindinu kanthu konse, ndipo zochita zanu nzopandapake. Amene amakupembedzaniyo amandinyansa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, inu muli achabe, ndi ntchito yanu yachabe; wonyansa ali iye amene asankha inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu sindinu kanthu ndipo zochita zanu nʼzopandapake; amene amapembedza inu ali ngati chinthu chokanidwa chifukwa ndi choyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, inu muli acabe, ndi nchito yanu yacabe; wonyansa ali iye amene asankha inu.