Isaiah 41:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi, milungu yonseyi njachabe, zochita zake si kanthu konse. Mafano ake osungunula ali ngati mphepo yachabechabe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, iwo onse, ntchito zao zikhala zopanda pake ndi zachabe; mafano ao osungunula ndiwo mphepo ndi masokonezo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, milungu yonseyi ndi yachinyengo! Zochita zawo si kanthu konse; mafano awo ali ngati mphepo yachabechabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, iwo onse, nchito zao zikhala zopanda pace ndi zacabe; mafano ao osungunula ndiwo mphepo ndi masokonezo.