Isaiah 42:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndani ali wakhungu osakhala mtumiki wanga? Ndani ali gonthi ngati wamthenga amene ndikumtuma? Kodi ndani ali wakhungu ngati wokhulupirika wanga? Ndani ali gonthi ngati mtumiki wa Chauta?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani ali wakhungu, koma mtumiki wanga? Pena wagonthi, monga mthenga wanga, amene ndimtumiza? Ndani ali wakhungu monga bwenzi langa, ndi wakhungu monga mtumiki wa Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ali wosaona ndani, si mtumiki wanga kodi? Ndipo ndani ali wosamva ngati mthenga amene ndamutuma? Kodi ndani ali wosaona ngati uja ndinachita naye pangano, kapena wosaona ndani ngati mtumiki wa Yehova?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani ali wakhungu, koma mtumiki wanga? pena wagonthi, monga mthenga wanga, amene ndimtumiza? ndani ali wakhungu monga bwenzi langa, ndi wakhungu monga mtumiki wa Yehova?