Isaiah 42:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha chilungamo chake, Chauta adafunitsitsa kuti malamulo ake akhale opambana ndi aulemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinakondweretsa Yehova chifukwa cha chilungamo chake kukuza chilamulo, ndi kuchilemekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chinamukomera Yehova chifukwa cha chilungamo chake, kapena lamulo lake kukhala lalikulu ndi lopambana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinakondweretsa Yehova cifukwa ca cilungamo cace kukuza cilamulo, ndi kucilemekeza.