Isaiah 42:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi alipo wina mwa inu amene adzamvetsere zimenezi? Ndani adzatchere khutu ndi kuzisamala kutsogolo kuno?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani mwa inu adzatchera khutu lake pamenepo? Amene adzamvera ndi kumva nthawi yakudza?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani wa inu amene adzamvetsera zimenezi kapena kutchera khutu ndi kumva za mʼtsogolomo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani mwa inu adzachera khutu lace pamenepo? amene adzamvera ndi kumva nthawi yakudza?