Isaiah 43:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Koma simudapemphere kwa Ine, inu am'banja la Yakobe, mudatopa nane, inu Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komabe iwe sunandiitane Ine, Yakobo; koma iwe walema ndi Ine, Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Komatu simunapemphera kwa Ine, Inu a mʼbanja la Yakobo, munatopa nane, Inu Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komabe iwe sunandiitane Ine, Yakobo; koma iwe walema ndi Ine, Israyeli.