Isaiah 43:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu akunena kuti, “Itanani anthu anga ku bwalo la milandu. Maso ali nawo, koma sakupenya. Makutu ali nawo, koma sakumva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tulutsani anthu akhungu, amene ali ndi maso, ndi agonthi, amene ali ndi makutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tulutsa anthu amene ali nawo maso koma sakupenya, anthu amene ali nawo makutu koma sakumva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Turutsani anthu akhungu, amene ali ndi maso, ndi agonthi, amene ali ndi makutu.