Isaiah 44:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Mverani tsopano, inu am'banja la Yakobe. Inu Aisraele, ndinu atumiki anga, osankhidwa anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsopano, imva Yakobo, mtumiki wanga, ndi Israele, amene ndakusankha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Mvera tsopano, iwe Yakobo, mtumiki wanga, Israeli, amene ndinakusankha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsopano, imva Yakobo, mtumiki wanga, ndi Israyeli, amene ndakusankha;