Isaiah 44:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adzakula bwino ngati udzu wothirira bwino, ngati misondodzi yomera m'mbali mwa mitsinje.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo iwo adzaphuka pakati pa udzu, ngati msondodzi m'mphepete mwa madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzakula ngati udzu wothirira bwino ndi ngati bango lomera mʼmbali mwa mitsinje ya madzi oyenda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo iwo adzaphuka pakati pa maudzu, ngati msondodzi m'mphepete mwa madzi.