Isaiah 45:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa wofunsa bambo wake kuti, “Mwabereka chiyani,” kapena mai wake kuti, “Mwabala chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka kwa iye amene ati kwa atate wake, Kodi iwe ubalanji? Pena kwa mkazi, Ulikusauka ninji iwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa wofunsa abambo ake kuti, ‘Kodi munabereka chiyani?’ Kapena amayi ake kuti, ‘Kodi mufuna kubereka chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka kwa iye amene ati kwa atate wace, Kodi iwe ubalanji? pena kwa mkazi, Ulikusauka ninji iwe?