Isaiah 46:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku la chipulumutso ndalisendeza pafupi, layandikira, sindidzachedwa kukupulumutsani. Ndidzapulumutsa Ziyoni, ndipo ndidzapatsa dziko la Israele ulemerero.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiyandikizitsa chifupi chilungamo changa sichidzakhala patali, ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa; ndipo ndidzaika chipulumutso m'Ziyoni, cha kwa Israele ulemerero wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikubweretsa pafupi tsiku la chipulumutso changa; sichili kutali. Tsikulo layandikira ndipo sindidzachedwa kukupulumutsani ndi kupereka ulemerero wanga kwa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiyandikizitsa cifupi cilungamo canga sicidzakhala patari, ndipo cipulumutso canga sicidzacedwa; ndipo ndidzaika cipulumutso m'Ziyoni, ca kwa Israyeli ulemerero wanga.