Isaiah 47:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimo m'mene adzakuthandizire anthuwo amene wakhala ukugwira nao ntchito ndi kuchita nao malonda chiyambire cha ubwana wako. Onsewo adzangomwazikana, sipadzakhala ndi mmodzi yemwe wokupulumutsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zinthu zomwe unagwira ntchito yake, zidzatero nawe; iwo amene anachita malonda ndi iwe chiyambire pa ubwana wako, adzayenda yense kunka kumalo kwake; sipadzakhala wopulumutsa iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umu ndi mmene adzachitire amatsenga, anthu amene wakhala ukugwira nawo ntchito ndi kuchita nawo malonda chiyambire cha ubwana wako. Onse adzamwazika ndi mantha, sipadzakhala ndi mmodzi yemwe wokupulumutsa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zinthu zomwe unagwira nchito yace, zidzatero nawe; iwo amene anacita malonda ndi iwe ciyambire pa ubwana wako, adzayenda yense kunka kumalo kwace; sipadzakhala wopulumutsa iwe.