Isaiah 47:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuuza Babiloni kuti, “Khala chete ndi kuloŵa mu mdima, iwe namwali, Kaldeya. Sadzakutchulanso mfumukazi ya maufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khala iwe chete, lowa mumdima, mwana wamkazi wa Ababiloni; pakuti sudzatchedwanso mkazi wa maufumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Khala chete, ndipo lowa mu mdima, iwe namwali, Kaldeya; chifukwa sadzakutchulanso mfumukazi ya maufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khala iwe cete, lowa mumdima, mwana wamkazi wa Akasidi; pakuti sudzachedwanso mkazi wa maufumu.