Isaiah 48:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha ulemu wanga, ulemu wanga wokha, ndiye ndimachita zonse. Ndingalole bwanji kuti dzina langa linyozeke? Ulemerero wanga sindidzapatsa wina ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha Ine ndekha, chifukwa cha Ine ndekha ndidzachita ichi, pakuti dzina langa lidetsedwerenji? Ndi ulemerero wanga sindidzaupereka kwa wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha ulemu wanga, chifukwa cha ulemu wanga Ine ndikuchita zimenezi. Ndingalole bwanji kuti ndinyozeke? Ulemerero wanga sindidzawupereka kwa wina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca Ine ndekha, cifukwa ca Ine ndekha ndidzacita ici, pakuti dzina langa lidetsedwerenji? ndi ulemerero wanga sindidzaupereka kwa wina.